Miyambo 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma amene amandinyalanyaza amadzipweteka yekha,Ndipo amene amadana ndi ine amakonda imfa.”+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:36 Nsanja ya Olonda,3/15/2001, tsa. 28