Miyambo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Amene amalangiza wonyoza amachititsidwa manyazi,+Ndipo aliyense wodzudzula woipa adzavulazidwa. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:7 Nsanja ya Olonda,5/15/2001, ptsa. 29-30