Miyambo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usadzudzule wonyoza chifukwa angadane nawe.+ Dzudzula munthu wanzeru ndipo adzakukonda.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:8 Nsanja ya Olonda,5/15/2001, ptsa. 29-30