Miyambo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Nsanja ya Olonda,5/15/2001, tsa. 30
9 Pereka malangizo kwa munthu wanzeru ndipo adzawonjezera nzeru zake.+ Phunzitsa munthu wolungama ndipo adzapitiriza kuphunzira.