Miyambo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa ine ndidzachulukitsa masiku a moyo wako,+Ndipo ndidzawonjezera zaka za moyo wako. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Nsanja ya Olonda,5/15/2001, tsa. 30