Miyambo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova sadzachititsa kuti munthu wolungama akhale ndi njala,+Koma anthu oipa sadzawapatsa zimene amalakalaka. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:3 Nsanja ya Olonda,7/15/2001, tsa. 24
3 Yehova sadzachititsa kuti munthu wolungama akhale ndi njala,+Koma anthu oipa sadzawapatsa zimene amalakalaka.