Miyambo 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwana wochita zinthu mozindikira amatuta zokolola mʼchilimwe,Koma mwana wochititsa manyazi amakhala ali mʼtulo tofa nato pa nthawi yokolola.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:5 Nsanja ya Olonda,7/15/2001, tsa. 25
5 Mwana wochita zinthu mozindikira amatuta zokolola mʼchilimwe,Koma mwana wochititsa manyazi amakhala ali mʼtulo tofa nato pa nthawi yokolola.+