Miyambo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anzeru ndi amene amapitiriza kuphunzira zinthu zamtengo wapatali,+Koma pakamwa pa wopusa pamachititsa kuti awonongedwe.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:14 Nsanja ya Olonda,7/15/2001, tsa. 27
14 Anzeru ndi amene amapitiriza kuphunzira zinthu zamtengo wapatali,+Koma pakamwa pa wopusa pamachititsa kuti awonongedwe.+