Miyambo 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu wolemera amaona kuti chuma chake chili* ngati mzinda wokhala ndi mpanda wolimba. Koma anthu osauka amavutika chifukwa cha umphawi wawo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:15 Nsanja ya Olonda,9/15/2001, ptsa. 24-25
15 Munthu wolemera amaona kuti chuma chake chili* ngati mzinda wokhala ndi mpanda wolimba. Koma anthu osauka amavutika chifukwa cha umphawi wawo.+