Miyambo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa munthu wopusa, kuchita khalidwe lochititsa manyazi kuli ngati masewera,Koma munthu wozindikira amakhala ndi nzeru.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:23 Nsanja ya Olonda,9/15/2001, ptsa. 26-273/15/1997, tsa. 13
23 Kwa munthu wopusa, kuchita khalidwe lochititsa manyazi kuli ngati masewera,Koma munthu wozindikira amakhala ndi nzeru.+