Miyambo 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mphepo yamkuntho ikawomba woipa amawonongedwa,+Koma wolungama ali ngati maziko mpaka kalekale.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:25 Nsanja ya Olonda,9/15/2001, tsa. 275/15/1987, tsa. 29