Miyambo 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kuopa Yehova kumatalikitsa moyo,+Koma zaka za anthu oipa zidzafupikitsidwa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:27 Nsanja ya Olonda,9/15/2001, tsa. 27