Miyambo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu amene amakonda malangizo* amakondanso kudziwa zinthu,+Koma amene amadana ndi kudzudzulidwa ndi wosaganiza bwino.*+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, ptsa. 28-29
12 Munthu amene amakonda malangizo* amakondanso kudziwa zinthu,+Koma amene amadana ndi kudzudzulidwa ndi wosaganiza bwino.*+