Miyambo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova amasangalala ndi munthu wabwino,Koma munthu amene amakonza mapulani ochita zinthu zoipa, Mulungu amamuweruza kuti ndi wolakwa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:2 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, tsa. 28
2 Yehova amasangalala ndi munthu wabwino,Koma munthu amene amakonza mapulani ochita zinthu zoipa, Mulungu amamuweruza kuti ndi wolakwa.+