Miyambo 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkazi wamakhalidwe abwino ndi chisoti cha ulemu kwa mwamuna wake,+Koma mkazi wochita zinthu zochititsa manyazi ali ngati matenda amene amawoletsa mafupa a mwamunayo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:4 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, ptsa. 29-30
4 Mkazi wamakhalidwe abwino ndi chisoti cha ulemu kwa mwamuna wake,+Koma mkazi wochita zinthu zochititsa manyazi ali ngati matenda amene amawoletsa mafupa a mwamunayo.+