Miyambo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a anthu oipa ali ngati msampha wakupha,*+Koma pakamwa pa anthu owongoka mtima pamawapulumutsa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:6 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, tsa. 30
6 Mawu a anthu oipa ali ngati msampha wakupha,*+Koma pakamwa pa anthu owongoka mtima pamawapulumutsa.+