Miyambo 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Amene amalima munda wake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+Koma amene amafunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:11 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, tsa. 31/15/2003, tsa. 31
11 Amene amalima munda wake adzakhala ndi chakudya chokwanira,+Koma amene amafunafuna zinthu zopanda pake ndi wopanda nzeru.