Miyambo 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu amasangalala ndi zinthu zabwino chifukwa cha mawu ake abwino,*+Ndipo ntchito za manja ake zidzamupindulira. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:14 Nsanja ya Olonda,3/15/2003, tsa. 27
14 Munthu amasangalala ndi zinthu zabwino chifukwa cha mawu ake abwino,*+Ndipo ntchito za manja ake zidzamupindulira.