Miyambo 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu woona mtima akamapereka umboni amalankhula zoona,*Koma mboni yonama imanena zachinyengo. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:17 Nsanja ya Olonda,3/15/2003, tsa. 27