Miyambo 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Milomo imene imalankhula zoona idzakhalapo mpaka kalekale,+Koma lilime labodza lidzangokhalapo kwa kanthawi kochepa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:19 Nsanja ya Olonda,2/1/2007, tsa. 73/15/2003, tsa. 28
19 Milomo imene imalankhula zoona idzakhalapo mpaka kalekale,+Koma lilime labodza lidzangokhalapo kwa kanthawi kochepa.+