Miyambo 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu waulesi akamasaka sathamangitsa nyama imene akufuna kupha,+Koma khama ndi chuma chamtengo wapatali cha munthu. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:27 Nsanja ya Olonda,3/15/2003, tsa. 30
27 Munthu waulesi akamasaka sathamangitsa nyama imene akufuna kupha,+Koma khama ndi chuma chamtengo wapatali cha munthu.