Miyambo 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amayangʼanira pakamwa pake* amateteza moyo wake,+Koma amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Nsanja ya Olonda,9/15/2003, tsa. 22
3 Amene amayangʼanira pakamwa pake* amateteza moyo wake,+Koma amene amatsegula kwambiri pakamwa pake adzawonongeka.+