Miyambo 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Munthu wochenjera amadziwa zimene akuchita,+Koma wopusa amaonetsa uchitsiru wake wonse.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:16 Nsanja ya Olonda,7/15/2004, tsa. 28