Miyambo 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mboni yokhulupirika sinama,Koma mboni yabodza imalankhula zabodza zokhazokha.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:5 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, ptsa. 27-28