Miyambo 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nzeru zimathandiza munthu wochenjera kuzindikira njira imene akuyenda,Koma anthu opusa amapusitsika* ndi kupusa kwawo komwe.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:8 Nsanja ya Olonda,11/15/2004, tsa. 29
8 Nzeru zimathandiza munthu wochenjera kuzindikira njira imene akuyenda,Koma anthu opusa amapusitsika* ndi kupusa kwawo komwe.+