Miyambo 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu wa mtima wosakhulupirika adzakumana ndi zotsatira za zochita zake,+Koma munthu wabwino amapeza mphoto chifukwa cha zochita zake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:14 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, tsa. 185/15/1987, tsa. 29
14 Munthu wa mtima wosakhulupirika adzakumana ndi zotsatira za zochita zake,+Koma munthu wabwino amapeza mphoto chifukwa cha zochita zake.+