Miyambo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu amene amanyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,Koma wosangalala ndi munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:21 Nsanja ya Olonda,7/15/2005, tsa. 2010/15/1986, ptsa. 10-24
21 Munthu amene amanyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,Koma wosangalala ndi munthu amene amakomera mtima anthu onyozeka.+