Miyambo 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Munthu womvetsa zinthu salankhula modzitama kuti ali ndi nzeru,+Koma munthu wopusa, nthawi zonse amalengeza zimene akudziwa. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:33 Nsanja ya Olonda,9/15/2005, tsa. 15
33 Munthu womvetsa zinthu salankhula modzitama kuti ali ndi nzeru,+Koma munthu wopusa, nthawi zonse amalengeza zimene akudziwa.