Miyambo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+Koma pakamwa pa zitsiru pamangolankhula mawu opusa. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Nsanja ya Olonda,7/1/2006, tsa. 14
2 Lilime la anthu anzeru limalankhula zabwino zimene anthuwo akudziwa,+Koma pakamwa pa zitsiru pamangolankhula mawu opusa.