Miyambo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mtima wachimwemwe umapangitsa kuti nkhope izioneka yosangalala,Koma munthu sasangalala ngati mtima ukumupweteka.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:13 Nsanja ya Olonda,7/1/2006, tsa. 16
13 Mtima wachimwemwe umapangitsa kuti nkhope izioneka yosangalala,Koma munthu sasangalala ngati mtima ukumupweteka.+