Miyambo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+Kusiyana ndi kukhala ndi chuma chambiri koma uli ndi nkhawa.*+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:16 Nsanja ya Olonda,8/1/2006, tsa. 16
16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+Kusiyana ndi kukhala ndi chuma chambiri koma uli ndi nkhawa.*+