Miyambo 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndi bwino kudya zamasamba koma pali chikondi,+Kusiyana ndi kudya nyama ya ngʼombe yamphongo yonenepa* koma pali chidani.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:17 Nsanja ya Olonda,8/1/2006, tsa. 16
17 Ndi bwino kudya zamasamba koma pali chikondi,+Kusiyana ndi kudya nyama ya ngʼombe yamphongo yonenepa* koma pali chidani.+