Miyambo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya munthu waulesi ili ngati mpanda wa mitengo yaminga,+Koma njira ya munthu wowongoka mtima ili ngati msewu wosalazidwa bwino.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:19 Nsanja ya Olonda,8/1/2006, tsa. 17
19 Njira ya munthu waulesi ili ngati mpanda wa mitengo yaminga,+Koma njira ya munthu wowongoka mtima ili ngati msewu wosalazidwa bwino.+