Miyambo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu amasangalala akapereka yankho labwino,*+Ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:23 Nsanja ya Olonda,8/1/2006, ptsa. 18-195/15/1987, tsa. 29
23 Munthu amasangalala akapereka yankho labwino,*+Ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+