Miyambo 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense amene amakana malangizo amanyoza moyo wake,+Koma amene amamvetsera akadzudzulidwa amakhala wozindikira.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:32 Nsanja ya Olonda,8/1/2006, tsa. 20
32 Aliyense amene amakana malangizo amanyoza moyo wake,+Koma amene amamvetsera akadzudzulidwa amakhala wozindikira.+