Miyambo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Koma Yehova ndi amene amayesa mitima.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:3 Galamukani!,8/8/1990, tsa. 15
3 Siliva amamuyengera mʼmbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera mungʼanjo,+Koma Yehova ndi amene amayesa mitima.+