Miyambo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kuyambitsa ndewu kuli ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.*Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:14 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Buku la Onse, tsa. 26
14 Kuyambitsa ndewu kuli ngati kuboola damu kuti madzi atulukemo.*Choncho mkangano usanabuke, chokapo.+