Miyambo 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wozindikira amakhala ndi cholinga choti apeze nzeru,Koma maso a munthu wopusa amangoyendayenda mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:24 Nsanja ya Olonda,9/15/2006, tsa. 19
24 Munthu wozindikira amakhala ndi cholinga choti apeze nzeru,Koma maso a munthu wopusa amangoyendayenda mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+