Miyambo 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kusangalatsa mʼbale amene walakwiridwa nʼkovuta kwambiri kuposa kulanda mzinda wokhala ndi mpanda wolimba,+Ndipo mikangano ingathe kulekanitsa anthu ngati mageti otseka a mzinda wolimba.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:19 Nsanja ya Olonda,9/15/2006, tsa. 192/1/1994, tsa. 32
19 Kusangalatsa mʼbale amene walakwiridwa nʼkovuta kwambiri kuposa kulanda mzinda wokhala ndi mpanda wolimba,+Ndipo mikangano ingathe kulekanitsa anthu ngati mageti otseka a mzinda wolimba.+