Miyambo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mimba ya munthu imakhuta zipatso za mawu otuluka pakamwa pake.+Iye amakhuta zokolola za milomo yake.
20 Mimba ya munthu imakhuta zipatso za mawu otuluka pakamwa pake.+Iye amakhuta zokolola za milomo yake.