Miyambo 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Imfa ndiponso moyo zili mumphamvu ya lilime,+Ndipo amene amakonda kuligwiritsa ntchito adzadya zipatso zake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:21 Nsanja ya Olonda,3/1/2000, tsa. 17
21 Imfa ndiponso moyo zili mumphamvu ya lilime,+Ndipo amene amakonda kuligwiritsa ntchito adzadya zipatso zake.+