Miyambo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+Ndipo mkazi wolongolola* ali ngati denga limene silisiya kudontha.+
13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+Ndipo mkazi wolongolola* ali ngati denga limene silisiya kudontha.+