Miyambo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu amene amamwa vinyo wambiri amayamba kunyoza+ ndipo amene amamwa mowa wambiri amachita zosokoneza.+Aliyense amene amasochera ndi zinthu zimenezi alibe nzeru.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:1 Nsanja ya Olonda,12/1/2004, ptsa. 19-215/1/2000, tsa. 198/1/1987, ptsa. 3-45/15/1987, tsa. 29
20 Munthu amene amamwa vinyo wambiri amayamba kunyoza+ ndipo amene amamwa mowa wambiri amachita zosokoneza.+Aliyense amene amasochera ndi zinthu zimenezi alibe nzeru.+