Miyambo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumu ikakhala pampando wachifumu kuti iweruze,+Maso ake amazindikira* anthu onse oipa.+