Miyambo 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndi ndani anganene kuti: “Ndayeretsa mtima wanga.+Ndine woyera ku tchimo langa”?+