Miyambo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Usamakonde tulo chifukwa ungasauke.+ Tsegula maso ako ndipo udzakhala ndi chakudya chambiri.+