Miyambo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wonenera anzake zoipa amayendayenda nʼkumaulula zinsinsi.+Usamagwirizane ndi munthu amene amakonda kunena miseche.*
19 Wonenera anzake zoipa amayendayenda nʼkumaulula zinsinsi.+Usamagwirizane ndi munthu amene amakonda kunena miseche.*