Miyambo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aliyense amene amatemberera bambo ake komanso mayi ake,Nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+