Miyambo 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonamaKuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira komanso msampha wakupha.*+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:6 Nsanja ya Olonda,4/15/1987, tsa. 24 Galamukani!,4/8/1988, tsa. 20
6 Kupeza chuma pogwiritsa ntchito lilime lonamaKuli ngati nkhungu imene imachoka mofulumira komanso msampha wakupha.*+