Miyambo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense amene amatseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,Nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:13 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2021, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,3/15/1993, tsa. 20
13 Aliyense amene amatseka khutu lake kuti asamve kudandaula kwa munthu wonyozeka,Nayenso adzaitana koma sadzayankhidwa.+